Creation Science Information & Links!
Mungayambe pamenepo
Mafunso ndi Mayankho
Malo olumikizana
EN Nkhani zolembedwa
Mabuku
Zithunzithunzi
Mau ojambulidwa, MP3
Zithunzithunzi za videyo

Genesis 1:1  "Pachiyambi Mulungu adalenga za kumwamba ndi dziko lapansi."

Yohane 1:1  "Pachiyambi pa zonse Iye amene amatchedwa
dzina loti Mau anali alipo kale. Anali ndi Mulungu, ndipo anali ndiye Mulungu."

Chiphunzitso cha Chilengedwe chimafotokoza kuti anthu, dziko lapansi, ndiponso zolengedwa zina zonse zinapangidwa ndi Mulungu basi.  Zimenezi sizinatuluke mwakuphulika mwangozi kapena kupezeka mwa mwai chabe.

Ife timakhala pa dziko limene linapangidwa mwaukatswiri ndi Mulungu, amene amayang’anira ndi kusamala zonsezi ndi mphamvu zake mwanzeru. Ife, pamodzi ndi anthu onse, timachitira umboni zabwino ndi zokoma zonse zimene Mulungu anazilenga. Taganizani za izitu: Kodi zanzeru, maphunziro, nyengo za pa chaka, chikondi, maluso, zipangizo—zonsezi, zinachokera mwa izo zokha? Kapena zinadzilenga zokha kodi?

Mwa anthu onse okhala padzikoli, ife a makono sitingadzikanire kunena kuti sitizindikira kuti Mlengi wanzeru alipo, amene iye yekha analenga zonsezi.  N’chifukwa chake ife tiyenera kukhala odabwa ndiponso oopa—osati anthu okayika kapena okana izi.

Zaka zikwi zitatu zapitazo Mfumu Davide analemba izi pa Salimo 8:3-4:  "Ndikamayang’ana ku thambo lanu limene mudapanga ndi manja anu, Ndikamaona mwezi ndi nyenyezi zimene mudazikhazika kumeneko, ndimadzifunsa kuti, 'Kodi munthu nchiyani kuti muzimkumbukira? Nanga mwana wa munthu nchiyani kuti muzimusamalira?' "

Nyanja  Chichewa  Nyasa  ―
齐切瓦
chewa
الشيوا
―  Chewa
 MENU
NY Nkhani zolembedwa
Buku Loyera
Kids&Teens

Zithunzi za m’Baibulo zokwanira 220 zolembedwa ndi Doré
 
Nkhani za m’Baibulo m’zithunzi zokwanira 250

MALO ENA A PA ‘WEB’ MU CHICHEWA OKHUDZANA
NDI MAPHUNZIRO OZAMA A CHILENGEDWE

Other Web Sites in Chinyanja with Creation Science


... None yet ...     Go to: International Links

Buku Loyera  •  Holy Bible  •  Chipangano Chakale ndi Chatsopano
Buku Lopatulika
Chichewa Buku Lopatulika
Blue-Letter

The Christian Gospel Message
Lord Jesus Christ · Matthew 6
10 Commandments
2 Commandments
Chikhulupiriro cha Atumwi
The Apostles' Creed - in Nyanja
Psalms
1 • 51 • 100 • 150
Bible Books Grid
Received Text or Critical Text

  Zothandiza zina za Chikhristu
  More Christian Resources

   Kodi Munamva
Malamulo Anai a Uzimu?
DenSu Ministries - Free Book
 


  "Njira Ya kwa Mulungu"

  "Satana Kutsutsana ndi KRISTU"

God's Story: From Creation to Eternity
God's Story
Got Questions?
ChiChewa
SGM LifeWords
English
Fellowship Tract League
chiNjanya
ChristianAnswers.Net

Uwu Unali Moyo Wako!
 (This was your life!)
Amakonda Iwe Ndi Ndani?
 (Who Loves You?)
The Light of the World
Sm · 190MB
Lg · 675MB
English  -  78 Minutes
Kodi Akatolika ndi Akhristu?
Are Roman Catholics Christians?
Chilombocho
The Beast
Onamizidwawo
The Deceived
Mawu Anasandulika Thupi
The Word Became Flesh
Miyambo Yomaliza
Last Rites
Ulendo Wautali
The Long Trip
Njira Imodzi!
One Way

JESUS FILM
PROJECT

Audio Gospel  •  Good News


The "Olivet Discourse" about the
End Times - all 3 accounts start -
  with a warning from Jesus!
Matt. 24:4b  "Take heed that no man deceive you."
Mark 13:5b  "Take heed lest any man deceive you."
Luke 21:8a  "Jesus said, Take heed that ye be not deceived."
We live in a world with daily false "News" - intended to deceive us!  Isaiah 5:20  Look for REAL NEWS & TRUTH!.  (And let's pray for wisdom!  James 1:5)
NEWS:

World Net


Review

Post - News
Voice of
the Martyrsдети
Kids
الأطفال
Kinder
Children & Teenagers / Kids & 
Teens / 孩子 & Подростки
青少年
Adolescents
किशोर
Youth

     Certificate of Debt  •  Paid in Full!
Has anyone ever shown you from the Bible how you can know for certain that you will go to heaven when you die?
The word “Gospel” means “good news.” It is the good news of how you can have a loving, personal relationship with God that gives meaning and purpose to this life, and, at the same time, gives you the certainty that you will spend eternity with Him in heaven. Say a sinner’s prayer!
Come forward and confess Christ publicly!
Repent and be baptized!
Give your heart to God!
Make a personal commitment to Christ!
Deny yourself, take up your cross, and follow Christ!
Invite Jesus into your heart!
Turn your life over to Jesus!
Pray to receive Christ!
Make Christ the Lord of your life!
Turn from your sins to God!
Put Christ on the throne of your life!

 

Main Links Page  -  g2yx82.cn/topbar/links.htm
 
— CHEWA; NYANJA; ChiChewa; ChiNyanja —   Dialects:  Town Nyanja
This language is spoken in:   Malawi; Zambia; Zimbabwe; Mozambique
Maphunziro ena ofotokozera za nkhani za ‘sayansi’ alipo pano, makamaka okhudza izi::
‘Biology’ [Za moyo wa nyama ndi zomera], ‘Geology’ [Za nthaka ndi miyala yake],
‘Paleontology’ [Za mafupa a zamoyo zakale], ‘Astronomy’ [Za nyenyezi za mlengalenga],
‘Intelligent Design’ [Za chilengedwe chopangidwa mwa ukatswiri],
‘Evolution’ [Za kusinthika kwa chilengedwe], Za Adamu ndi Hava, Chombo cha Nowa,
Nyengo yozizira pa dziko lapansi, Munda wa Edeni, ndiponso Za mbiri ya dziko lapansi.
Nkhani m’Chingerezi za:  Zirombo za kale [madayinasawa]
Nkhani m’Chingerezi za:  Nyamalikiti/Kadyansongo
Nkhani m’Chingerezi za:  Gogomole
Nkhani m’Chingerezi za:  Mileme
 
-- Nkhani zina za m’Chingerezi zili PANO --

Mungayambe pamenepo
Mafunso ndi Mayankho
Malo olumikizana
EN Nkhani zolembedwa
Mabuku
Zithunzithunzi
Mau ojambulidwa, MP3
Zithunzithunzi za videyo

幸运飞艇9码稳赢公式竞猜中心 幸运飞艇3把必中 二分飞艇计划预测 精准免费的幸运飞艇神计划计划 飞艇计划app开奖 幸运飞艇属于福彩不属于 飞艇1期计划 辛运飞艇精准在线8码计划 幸运飞艇开奖结果纪录完整版 幸运飞艇是哪国的 幸运飞艇【上恒达集团~HD161。COM~平台】 幸运飞艇【上恒达集团~HD161。COM~平台】 幸运飞艇【上恒达集团~HD161。COM~平台】 澳门百家乐【上恒达集团~HD161。COM~平台】 澳门百家乐【上恒达集团~HD161。COM~平台】 澳门百家乐【上恒达集团~HD161。COM~平台】 六合彩公司【上恒达集团~HD161。COM~平台】